Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 115:17 - Buku Lopatulika

17 Akufa salemekeza Yehova, kapena aliyense wakutsikira kuli chete:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Akufa salemekeza Yehova, kapena aliyense wakutsikira kuli chete:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Akufa satamanda Chauta otsikira ku dziko lachete satamanda Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Si anthu akufa amene amatamanda Yehova, amene amatsikira kuli chete;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 115:17
7 Mawu Ofanana  

M'mwazi mwanga muli phindu lanji, potsikira ine kudzenje? Ngati fumbi lidzayamika Inu? Ngati lidzalalikira choonadi chanu?


Yehova, musandichititse manyazi; pakuti ndafuulira kwa Inu, oipa achite manyazi, atonthole m'manda.


Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?


Ndalema nako kuusa moyo kwanga; ndiyandamitsa kama wanga usiku wonse; mphasa yanga ndiolobza ndi misozi yanga.


Adzasunga mapazi a okondedwa ake, koma oipawo adzawakhalitsa chete mumdima; pakuti palibe munthu adzapambana ndi mphamvu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa