Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 115:15 - Buku Lopatulika

15 Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Odalitsika inu a kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Akudalitseni Chauta, amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Mudalitsidwe ndi Yehova, Wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 115:15
13 Mawu Ofanana  

Pachiyambi Mulungu adalenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Ndipo anamdalitsa iye, nati, Abramu adalitsike ndi Mulungu Wamkulukulu, mlengi wa kumwamba ndi dziko lapansi;


Thandizo langa lidzera kwa Yehova, wakulenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Thandizo lathu lili m'dzina la Yehova, wolenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Yehova, ali mu Ziyoni, akudalitseni; ndiye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi.


Chipulumutso ncha Yehova; dalitso lanu likhale pa anthu anu.


Pakuti milungu yonse ya mitundu ya anthu ndiyo mafano, koma Yehova analenga zakumwamba.


nafuula nati, Anthuni, bwanji muchita zimenezi? Ifenso tili anthu a mkhalidwe wathu umodzimodzi ndi wanu, akulalikira kwa inu Uthenga Wabwino, wakuti musiye zinthu zachabe izi, nimutembenukire kwa Mulungu wamoyo, amene analenga zakumwamba ndi zapansi, ndi nyanja, ndi zonse zili momwemo:


osabwezera choipa ndi choipa, kapena chipongwe ndi chipongwe, koma penatu madalitso; pakuti kudzatsata ichi mwaitanidwa, kuti mukalandire dalitso.


ndi kunena ndi mau aakulu, Opani Mulungu, mpatseni ulemerero; pakuti yafika nthawi ya chiweruziro chake; ndipo mlambireni Iye amene analenga kumwamba ndi dziko lapansi ndi nyanja ndi akasupe amadzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa