Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 115:11 - Buku Lopatulika

11 Inu akuopa Yehova, khulupirirani Yehova; ndiye mthandizi wao ndi chikopa chao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Inu akuopa Yehova, khulupirirani Yehova; ndiye mthandizi wao ndi chikopa chao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Inu amene mumaopa Chauta, mkhulupirireni. Chauta ndiye mthandizi wanu ndi chishango chanu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Inu amene mumaopa Iye, dalirani Yehova; Iye ndiye thandizo lanu ndi chishango chanu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 115:11
11 Mawu Ofanana  

Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye.


Anene tsono Israele, kuti chifundo chake nchosatha.


Anene tsono iwo akuopa Yehova, kuti chifundo chake nchosatha.


A nyumba ya Israele inu, lemekezani Yehova: A nyumba ya Aroni inu, lemekezani Yehova:


Yehova akondwera nao akumuopa Iye, iwo akuyembekeza chifundo chake.


Inu akuopa Yehova, mumlemekeze; inu nonse mbumba ya Yakobo, mumchitire ulemu; ndipo muchite mantha ndi Iye, inu nonse mbumba ya Israele.


Taonani, diso la Yehova lili pa iwo akumuopa Iye, pa iwo akuyembekeza chifundo chake.


Wakuopa Yehova akhulupirira kolimba; ndipo ana ake adzakhala ndi pothawirapo.


Mau onse a Mulungu ali oyengeka; ndiye chikopa cha iwo amene amkhulupirira.


koma m'mitundu yonse, wakumuopa Iye ndi wakuchita chilungamo alandiridwa naye.


Ndipo mau anachokera kumpando wachifumu, ndi kunena, Lemekezani Mulungu wathu akapolo ake onse akumuopa Iye, aang'ono ndi aakulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa