Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 114:8 - Buku Lopatulika

8 amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi, nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 amene anasanduliza thanthwe likhale thawale lamadzi, nsangalabwi ikhale kasupe wamadzi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Iye amasandutsa thanthwe kukhala dziŵe lamadzi, amasandutsa mwala wolimba kukhala kasupe wa madzi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 amene anasandutsa thanthwe kukhala chitsime, thanthwe lolimba kukhala akasupe a madzi.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 114:8
8 Mawu Ofanana  

ndi mkate wochokera m'mwamba munawapatsa pa njala yao; ndi madzi otuluka m'thanthwe munawatulutsira pa ludzu lao, ndi kuwauza alowe, nalandire dziko limene mudakwezapo dzanja lanu kuwapatsa.


Anatsegula pathanthwe, anatulukamo madzi; nayenda pouma ngati mtsinje.


Asanduliza chipululu chikhale thawale, ndi dziko louma likhale akasupe a madzi.


Taona, ndidzaima pamaso pako pathanthwe mu Horebu; ndipo upande thanthwe, nadzatulukamo madzi, kuti anthu amwe. Ndipo Mose anachita chomwecho pamaso pa akulu a Israele.


Ndipo Mose anasamula dzanja lake, napanda thanthwe kawiri ndi ndodo; ndipo madzi anatulukamo ochuluka, ndi khamulo linamwa, ndi zoweta zao zomwe.


namwa onse chakumwa chauzimu chimodzimodzi; pakuti anamwa mwa thanthwe lauzimu lakuwatsata; koma thanthwelo ndiye Khristu.


amene anakutsogolerani m'chipululu chachikulu ndi choopsacho, munali njoka zamoto, ndi zinkhanira, mouma mopanda madzi; amene anakutulutsirani madzi m'thanthwe lansangalabwi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa