Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 114:7 - Buku Lopatulika

7 Unjenjemere, dziko lapansi iwe, pamaso pa Ambuye, pamaso pa Mulungu wa Yakobo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Unjenjemere, dziko lapansi iwe, pamaso pa Ambuye, pamaso pa Mulungu wa Yakobo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Njenjemera iwe dziko lapansi, chifukwa Chauta akubwera, zoonadi, akubwera Mulungu wa Yakobe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Njenjemera pamaso pa Ambuye iwe dziko lapansi, pamaso pa Mulungu wa Yakobo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 114:7
10 Mawu Ofanana  

Mizati ya thambo injenjemera, ndi kudabwa pa kudzudzula kwake.


Amene agwedeza dziko lapansi lichoke m'malo mwake, ndi mizati yake injenjemere.


amene apenyerera padziko lapansi, ndipo linjenjemera; akhudza mapiri, ndipo afuka.


Liu la bingu lanu linatengezanatengezana; mphezi zinaunikira ponse pali anthu; dziko lapansi linanjenjemera ndi kugwedezeka.


Anatulukitsa mitsinje m'thanthwe, inde anatsikitsa madzi ngati mitsinje.


Gwadirani Yehova moyera ndi mokometsetsa, njenjemerani pamaso pake, inu dziko lonse lapansi.


Kodi simundiopa Ine? Ati Yehova: simudzanthunthumira pamaso pa Ine, amene ndinaika mchenga chilekaniro cha nyanja, ndi lemba lamuyaya kuti isapitirirepo? Ndipo ngakhale mafunde ake achita gavigavi, alephera; ngakhale akokoma, sangathe kupitirirapo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa