Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 114:6 - Buku Lopatulika

6 Munatumphatumphiranji ngati nkhosa zamphongo, mapiri inu? Ngati anaankhosa, zitunda inu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Munatumphatumphiranji ngati nkhosa zamphongo, mapiri inu? Ngati anaankhosa, zitunda inu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Inu mapiri, chikukuvutani nchiyani, kuti muzilumphalumpha ngati nkhosa zamphongo? Nanga inu zitunda, mukulumphiranji ngati anaankhosa?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 inu mapiri, munalumphalumphiranji ngati nkhosa zazimuna, inu timapiri, ngati ana ankhosa?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 114:6
3 Mawu Ofanana  

Amene agwedeza dziko lapansi lichoke m'malo mwake, ndi mizati yake injenjemere.


Mapiri anatumphatumpha ngati nkhosa zamphongo, timapiri ngati anaankhosa.


Aitumphitsa monga mwanawang'ombe; Lebanoni ndi Sirioni monga msona wa njati.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa