Masalimo 114:5 - Buku Lopatulika5 Unathawanji nawe, nyanja iwe? Unabwereranji m'mbuyo, Yordani iwe? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Unathawanji nawe, nyanja iwe? Unabwereranji m'mbuyo, Yordani iwe? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Iwe nyanja, chikukuvuta nchiyani kuti uzithaŵa? Nanga iwe Yordani, ukubwerereranji m'mbuyo? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Nʼchifukwa chiyani iwe unathawa? iwe mtsinje wa Yorodani unabwereranji mʼmbuyo? Onani mutuwo |