Masalimo 109:28 - Buku Lopatulika28 Atemberere iwowa, koma mudalitse ndinu; pakuuka iwowa adzachita manyazi, koma mtumiki wanu adzakondwera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Atemberere iwowa, koma mudalitse ndinu; pakuuka iwowa adzachita manyazi, koma mtumiki wanu adzakondwera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Iwo atemberere, koma Inu mundidalitse. Ondiputa muŵachititse manyazi, koma ine mtumiki wanu ndisangalale. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Angathe kutemberera, koma Inu mudzadalitsa; pamene iwo andiputa adzachititsidwa manyazi, koma mtumiki wanu adzasangalala. Onani mutuwo |