Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 109:24 - Buku Lopatulika

24 Mabondo anga agwedezeka chifukwa cha kusala; ndi mnofu wanga waonda posowa mafuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Mabondo anga agwedezeka chifukwa cha kusala; ndi mnofu wanga waonda posowa mafuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Maondo anga afooka chifukwa chosala zakudya, thupi langa laonda ndi mutu womwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Mawondo anga afowoka chifukwa cha kusala zakudya, thupi langa lawonda ndi mutu wanga womwe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 109:24
11 Mawu Ofanana  

Fupa langa laumirira pa khungu langa ndi mnofu wanga, ndipo ndapulumuka ndili nazo nkhama za mano anga.


Ndathiridwa pansi monga madzi, ndipo mafupa anga onse anaguluka. Mtima wanga ukunga sera; wasungunuka m'kati mwa matumbo anga.


Ndipo ndinalira pa kusala kwa moyo wanga, koma uku kunandikhalira chotonza.


Ndipo chovala changa ndinayesa chiguduli, koma amandiphera mwambi.


Ndipo pamene Iye analibe kudya masiku makumi anai usana ndi usiku, pambuyo pake anamva njala.


m'chivutitso ndi m'cholemetsa, m'madikiro kawirikawiri, m'njala ndi ludzu, m'masalo a chakudya kawirikawiri, m'chisanu ndi umaliseche.


Mwa ichi limbitsani manja ogooka, ndi maondo olobodoka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa