Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 107:9 - Buku Lopatulika

9 Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pakuti akhutitsa mtima wolakalaka, nadzaza mtima wanjala ndi zabwino.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Chauta amapha ludzu la munthu womva ludzu, amamudyetsa zinthu zabwino munthu womva njala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 pakuti Iye wapha ludzu la munthu womva ludzu ndipo wakhutitsa wanjala ndi zinthu zabwino.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 107:9
11 Mawu Ofanana  

Ndidzadalitsatu chakudya chake; aumphawi ake ndidzawakhutitsa ndi mkate.


ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi.


Ozunzika adzadya nadzakhuta, adzayamika Yehova iwo amene amfuna, ukhale moyo mtima wako nthawi zonse.


Misona ya mkango isowa nimva njala, koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.


Idzani ananu ndimvereni ine, ndidzakulangizani zakumuopa Yehova.


Ndipo ndikhutitsa moyo wa ansembe ndi mafuta, ndipo anthu anga adzakhuta ndi zokoma zanga, ati Yehova.


Pakuti ndakhutidwa mtima wolema, ndadzazanso mtima uliwonse wachisoni.


Odala ali akumva njala ndi ludzu la chilungamo; chifukwa adzakhuta.


Anawakhutitsa anjala ndi zinthu zabwino, ndipo eni chuma anawachotsa opanda kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa