Masalimo 107:16 - Buku Lopatulika16 Popeza adaswa zitseko zamkuwa, nathyola mipiringidzo yachitsulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Popeza adaswa zitseko zamkuwa, nathyola mipiringidzo yachitsulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pajatu adathyola zitseko zamkuŵa, nadula paŵiri mipiringidzo yachitsulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 pakuti Iye amathyola zipata zamkuwa ndi kudula pakati mipiringidzo yachitsulo. Onani mutuwo |