Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 107:10 - Buku Lopatulika

10 Iwo akukhala mumdima ndi mu mthunzi wa imfa, omangika ndi kuzunzika ndi chitsulo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Iwo akukhala mumdima ndi mu mthunzi wa imfa, omangika ndi kuzunzika ndi chitsulo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ena adakhala mu mdima ali ndi chisoni, anali am'ndende ozunzika m'maunyolo achitsulo,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Ena anakhala mu mdima ndi mʼchisoni chachikulu, amʼndende ovutika mʼmaunyolo achitsulo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 107:10
13 Mawu Ofanana  

Motero Yehova anawafikitsira akazembe a khamu la nkhondo la mfumu ya Asiriya, namgwira Manase ndi zokowera, nammanga matangadza, namuka naye ku Babiloni.


Mdima ndi mthunzi wa imfa ziliyese laolao; mtambo ulikhalire; zonse zodetsa usana bii ziliopse.


Anapweteka miyendo yake ndi matangadza; anamgoneka mu unyolo;


kuti utsegule maso akhungu, utulutse am'nsinga m'ndende, ndi iwo amene akhala mumdima, atuluke m'nyumba ya kaidi.


Anthu amene anayenda mumdima, aona kuwala kwakukulu; iwo amene anakhala m'dziko la mthunzi wa imfa, kuwala kwatulukira kwa iwo.


Usandiseka, mdani wangawe; pakugwa ine ndidzaukanso; pokhala ine mumdima Yehova adzakhala kuunika kwanga.


Pomwepo mfumu inati kwa atumiki, Mumange iye manja ndi miyendo, mumponye kumdima wakunja; komweko kudzali kulira ndi kukukuta mano.


anthu akukhala mumdima adaona kuwala kwakukulu, ndi kwa iwo okhala m'malo a mthunzi wa imfa, kuwala kunatulukira iwo.


Kuwalitsira iwo okhala mumdima ndi mthunzi wa imfa; kulunjikitsa mapazi athu mu njira ya mtendere.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa