Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 106:4 - Buku Lopatulika

4 Mundikumbukire, Yehova, monga momwe muvomerezana ndi anthu anu; mundionetsa chipulumutso chanu:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Mundikumbukire, Yehova, monga momwe muvomerezana ndi anthu anu; mundionetsa chipulumutso chanu:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Chauta, mundikumbukire pamene mukukomera mtima anthu anu. Mundithandize pamene mukuŵapulumutsa,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Mundikumbukire Yehova, pamene mukuonetsa kukoma mtima kwanu kwa anthu anu, bwerani mudzandithandize pamene mukuwapulumutsa iwo,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 106:4
9 Mawu Ofanana  

Mundikumbukire Mulungu wanga mwa ichi, nimusafafanize zokoma zanga ndinazichitira nyumba ya Mulungu wanga, ndi maudikiro ake.


Ndipo ndinauza Alevi kuti adziyeretse, nabwere, nasunge pazipata kupatula tsiku la Sabata. Mundikumbukire ichinso, Mulungu wanga, ndi kundileka monga mwa chifundo chanu chachikulu.


ndi chopereka cha nkhuni pa nthawi zoikika, ndi wa zipatso zoyamba. Mundikumbukire, Mulungu wanga, chindikomere.


Mundikumbukire Mulungu, zindikomere zonse ndinachitira anthu awa.


Munditembenukire, ndi kundichitira chifundo, monga mumatero nao akukonda dzina lanu.


Musakumbukire zolakwa za ubwana wanga kapena zopikisana nanu. Mundikumbukire monga mwa chifundo chanu, chifukwa cha ubwino wanu, Yehova.


Ndipo ananena, Yesu, ndikumbukireni m'mene mulowa Ufumu wanu.


Simoni wabwereza kuti poyamba Mulungu anayang'anira amitundu, kuti atenge mwa iwo anthu a dzina lake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa