Masalimo 106:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo kumisasa anachita nao nsanje Mose ndi Aroni woyerayo wa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo kumisasa anachita nao nsanje Mose ndi Aroni woyerayo wa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Nthaŵi ina anthuwo adaachitira kaduka Mose ndi Aroni, mtumiki wopatulika wa Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Mʼmisasa, anachitira nsanje Mose ndi Aaroni, amene Yehova anadzipatulira. Onani mutuwo |