Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 106:12 - Buku Lopatulika

12 Pamenepo anavomereza mau ake; anaimbira chomlemekeza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Pamenepo anavomereza mau ake; anaimbira chomlemekeza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Tsono anthu ake adakhulupirira mau ake, naimba nyimbo zomtamanda.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Kenaka iwo anakhulupirira malonjezo ake ndi kuyimba nyimbo zamatamando.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 106:12
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Israele anaiona ntchito yaikulu imene Yehova anachitira Aejipito, ndipo anthuwo anaopa Yehova; nakhulupirira Yehova ndi mtumiki wake Mose.


Pamenepo Mose ndi ana a Israele anaimbira Yehova nyimbo iyi, nanena, ndi kuti, Ndidzaimbira Yehova pakuti wapambanatu; kavalo ndi wokwera wake anawaponya m'nyanja.


Ndipo za pathanthwe ndiwo amene, pakumva, alandira mau ndi kukondwera; koma alibe mizu; akhulupirira kanthawi, ndipo pa nthawi ya mayesedwe angopatuka.


ndi chimene anakuchitirani m'chipululu, kufikira munadza kumalo kuno;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa