Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 106:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo madziwo anamiza owasautsa; sanatsale mmodzi yense.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo madziwo anamiza owasautsa; sanatsale mmodzi yense.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndipo madzi adamiza adani ao onse, sadatsalepo ndi mmodzi yemwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Madzi anamiza adani awo, palibe mmodzi wa iwo anapulumuka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 106:11
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anawatsogolera mokhulupirika, kotero kuti sanaope; koma nyanja inamiza adani ao.


Ndipo Mose ananena ndi anthu, Musaope, chilimikani, ndipo penyani chipulumutso cha Yehova, chimene adzakuchitirani lero; pakuti Aejipito mwawaona lerowa, simudzawaonanso konse.


Munaombetsa mphepo yanu, nyanja inawamiza; anamira m'madzi aakulu ngati mtovu.


Pakuti akavalo a Farao analowa m'nyanja, ndi magaleta ake ndi apakavalo ake, ndipo Yehova anawabwezera madzi a m'nyanja; koma ana a Israele anayenda pouma pakati pa nyanja.


Nyanja inawamiza; anamira mozama ngati mwala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa