Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 106:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo anawapulumutsa m'dzanja la iye amene anawada, nawaombola kudzanja la mdani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo anawapulumutsa m'dzanja la iye amene anawada, nawaombola kudzanja la mdani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Motero adaŵapulumutsa kwa amaliwongo, naŵalanditsa ku mphamvu za adani ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Anawapulumutsa mʼdzanja la amaliwongo; anawawombola mʼdzanja la mdani.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 106:10
10 Mawu Ofanana  

Ndipo munagawanitsa nyanja pamaso pao, napita iwo pakati pa nyanja pouma, ndipo munaponya mozama owalondola, ngati mwala m'madzi olimba.


Atere oomboledwa a Yehova, amene anawaombola m'dzanja la wosautsa;


Natikwatula kwa otisautsa; pakuti chifundo chake nchosatha.


Mwa Mulungu tidzitamanda tsiku lonse, ndipo dzina lanu tidzaliyamika kosatha.


Chomwecho Yehova anapulumutsa Israele tsiku lomwelo m'manja a Aejipito; ndipo Israele anaona Aejipito akufa m'mphepete mwa nyanja.


Mwa chifundo chanu mwatsogolera anthu amene mudawaombola; mwamphamvu yanu mudawalondolera njira yakunka pokhala panu poyera.


Pakuti ndinakukwezani kukutulutsani m'dziko la Ejipito, ndi kuombola inu m'nyumba ya ukapolo; ndipo ndinatuma akutsogolereni Mose, Aroni, ndi Miriyamu.


ndi chochitira Iye nkhondo ya Ejipito, akavalo ao, ndi agaleta ao; kuti anawamiza m'madzi a Nyanja Yofiira, muja anakutsatani m'mbuyo, ndi kuti Yehova anawaononga kufikira lero lino;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa