Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 105:3 - Buku Lopatulika

3 Mudzitamandire ndi dzina lake loyera: mitima yao ya iwo ofunsira Yehova ikondwere.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mudzitamandire ndi dzina lake loyera: mitima yao ya iwo ofunsira Yehova ikondwere.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Munyadire dzina lake loyera. Ikondwe mitima ya anthu amene amapembedza Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Munyadire dzina lake loyera; mitima ya iwo amene amafunafuna Yehova ikondwere.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 105:3
13 Mawu Ofanana  

Pomlingirira Iye pandikonde; ndidzakondwera mwa Yehova.


Moyo wanga udzatamanda Yehova; ofatsa adzakumva nadzakondwera.


ndipo iwo akudziwa dzina lanu adzakhulupirira Inu; pakuti, Inu Yehova, simunawasiye iwo akufuna Inu.


Akundikonda ndiwakonda; akundifunafuna adzandipeza.


Ine sindinanene m'tseri m'malo a dziko la mdima; Ine sindinati kwa mbeu ya Yakobo, Mundifune Ine mwachabe; Ine Yehova ndinena chilungamo, ndinena zimene zili zoona.


Mwa Yehova mbeu yonse ya Israele idzalungamitsidwa ndi kudzikuza.


Yehova akhalira wabwino omlindirira, ndi moyo womfunafuna.


kuti thupi lililonse lisadzitamande pamaso pa Mulungu.


kuti monga mwalembedwa, Iye amene adzitamanda, adzitamande mwa Ambuye.


Koma kudzitamandira ine konsekonse, iai, koma mu mtanda wa Ambuye wathu Yesu Khristu, amene mwa Iye dziko lapansi lapachikidwira ine, ndi ine ndapachikidwira dziko lapansi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa