Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 105:2 - Buku Lopatulika

2 Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Imbirani Chauta, muimbireni nyimbo zomtamanda, lalikani za ntchito zake zodabwitsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Imbirani Iye, imbani matamando kwa Iyeyo; fotokozani za machitidwe ake onse odabwitsa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 105:2
17 Mawu Ofanana  

Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Ndipo ndidzalingalira ntchito yanu yonse, ndi kulingalirabe zimene munazichita Inu.


Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkulu ndani monga Mulungu?


Muimbireni Yehova nyimbo yatsopano; popeza anachita zodabwitsa: Dzanja lake lamanja, mkono wake woyera, zinamchitira chipulumutso.


Muimbireni Yehova zomlemekeza ndi zeze; ndi zeze ndi mau a salimo.


Ndipo kudzakhala, akakufunsa mwana wako masiku akudzawo ndi kuti, Ichi nchiyani? Ukanene naye, Yehova anatitulutsa mu Ejipito, m'nyumba ya ukapolo, ndi dzanja lamphamvu;


ndi kudzilankhulira nokha ndi masalimo, ndi mayamiko, ndi nyimbo zauzimu, kuimbira ndi kuimba m'malimba Ambuye mumtima mwanu;


Imvani mafumu inu; tcherani makutu, akalonga inu; ndidzamuimbira ine Yehova, inetu; ndidzamuimbira nyimbo, Yehova, Mulungu wa Israele.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa