Masalimo 104:26 - Buku Lopatulika26 M'mwemo muyenda zombo; ndi Leviyatani amene munamlenga aseweremo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 M'mwemo muyenda zombo; ndi Leviyatani amene munamlenga aseweremo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Zombo zimayendamo pamodzi ndi Leviyatani, chilombo chija chimene mudachilenga kuti chiziseŵera m'madzimo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Kumeneko sitima zapamadzi zimayenda uku ndi uku, ndiponso Leviyatani amene munamulenga kuti asewere kumeneko. Onani mutuwo |