Masalimo 104:25 - Buku Lopatulika25 Nyanja siyo, yaikulu ndi yachitando, m'mwemo muli zokwawa zosawerengeka; zamoyo zazing'ono ndi zazikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Nyanja siyo, yaikulu ndi yachitando, m'mwemo muli zokwawa zosawerengeka; zamoyo zazing'ono ndi zazikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Kuli nyanja yaikulu ndi yotambalala, yodzaza ndi zinthu zosaŵerengeka, zinthu zamoyo, zazing'ono ndi zazikulu zomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Kuli nyanja yayikulu ndi yotambalala, yodzaza ndi zolengedwa zosawerengeka, zamoyo zanu zazikulu ndi zazingʼono zomwe. Onani mutuwo |