Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 104:23 - Buku Lopatulika

23 Pamenepo munthu atulukira kuntchito yake, nagwiritsa kufikira madzulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

23 Pamenepo munthu atulukira kuntchito yake, nagwiritsa kufikira madzulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

23 Munthu amapita ku ntchito yake, amakagwira ntchito mpaka madzulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

23 Pamenepo munthu amapita ku ntchito yake, kukagwira ntchito yake mpaka madzulo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:23
5 Mawu Ofanana  

m'thukuta la nkhope yako udzadya chakudya, kufikira kuti udzabwerera kunthaka: chifukwa kuti m'menemo unatengedwa: chifukwa kuti ndiwe fumbi, ndi kufumbiko udzabwerera.


Tulo ta munthu wogwira ntchito ntabwino, ngakhale adya pang'ono ngakhale zambiri; koma kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo.


Wakubayo asabenso; koma makamaka agwiritse ntchito, nagwire ntchito yokoma ndi manja ake, kuti akhale nacho chakuchereza wosowa.


Ndipo taonani, munthu nkhalamba anachokera ku ntchito yake kumunda madzulo; munthuyu ndiye wa ku mapiri a Efuremu, nagonera ku Gibea; koma anthu pamenepo ndiwo Abenjamini.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa