Masalimo 104:22 - Buku Lopatulika22 Potuluka dzuwa, zithawa, zigona pansi m'ngaka mwao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Potuluka dzuwa, zithawa, zigona pansi m'ngaka mwao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Dzuŵa likamatuluka, imabwerera nkukagona m'mapanga mwake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Dzuwa limatuluka ndipo iyo imapita kukabisala; imabwerera kukagona pansi mʼmapanga awo. Onani mutuwo |