Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 104:21 - Buku Lopatulika

21 Misona ya mkango ibangula potsata nyama yao, nifuna chakudya chao kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Misona ya mkango ibangula potsata nyama yao, nifuna chakudya chao kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Misona ya mikango imabangula pofunafuna nyama, kupempha chakudya kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Mikango imabangula kufuna nyama, ndi kufunafuna chakudya chawo kuchokera kwa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:21
11 Mawu Ofanana  

Kodi ukhoza kusakira mkango waukazi nyama? Ndi kukwaniritsa chakudya cha misona,


Amkonzeratu khwangwala chakudya chake ndani, pamenepo ana ake afuulira kwa Mulungu, naulukauluka osowa chakudya?


Maso a onse ayembekeza Inu; ndipo muwapatsa chakudya chao m'nyengo zao.


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Misona ya mkango isowa nimva njala, koma iwo akufuna Yehova sadzasowa kanthu kabwino.


Pakuti Yehova atero kwa ine, Monga mkango, ndi mwana wa mkango wobangula pa nyama yake, sudzaopa mau a khamu la abusa oitanidwa kuupirikitsa, ngakhale kudzichepetsa wokha, chifukwa cha phokoso lao; motero Yehova wa makamu adzatsikira kumenyana nkhondo kuphiri la Ziyoni, ndi kuchitunda kwake komwe.


Ha! Nyama ziusa moyo, magulu a ng'ombe azimidwa; pakuti zisowa podyera; magulu a nkhosa omwe atha.


Inde nyama zakuthengo zilira kwa Inu; pakuti mitsinje yamadzi yaphwa, ndi moto wapsereza mabusa a m'chipululu.


Musamaopa, nyama zakuthengo inu; pakuti m'chipululu muphukanso msipu; pakuti mitengo ibala zipatso zao; mikuyu ndi mipesa ipatsa mphamvu zao.


Kodi mkango udzabangula m'nkhalango wosakhala nayo nyama? Kodi msona wa mkango udzalira m'ngaka mwake usanagwire kanthu?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa