Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 104:20 - Buku Lopatulika

20 Muika mdima ndipo pali usiku; pamenepo zituluka zilombo zonse za m'thengo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Muika mdima ndipo pali usiku; pamenepo zituluka zilombo zonse za m'thengo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Mumapanga mdima nukhala usiku, ndipo nyama zam'nkhalango zimatuluka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Inu mumabweretsa mdima nukhala usiku, ndipo zirombo zonse za ku nkhalango zimatuluka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:20
7 Mawu Ofanana  

Pakukhalabe masiku a dziko lapansi, nthawi yakubzala ndi yakukunkha, chisanu ndi mafundi, malimwe ndi msakasa, usana ndi usiku sizidzalekai.


Pakuti zamoyo zonse zakuthengo ndi zanga, ndi ng'ombe za pa mapiri zikwi.


Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa.


Ine ndilenga kuyera ndi mdima, Ine ndilenga mtendere ndi choipa, Ine ndine Yehova wochita zinthu zonse zimenezi.


Atero Yehova, Chifukwa cha zolakwa zitatu za ana a Amoni, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwake; popeza anatumbula akazi ali m'pakati a Giliyadi, kuti akuze malire ao;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa