Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 104:19 - Buku Lopatulika

19 Anaika mwezi nyengo zake; dzuwa lidziwa polowera pake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Anaika mwezi nyengo zake; dzuwa lidziwa polowera pake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Inu mudapanga mwezi kuti uzisiyanitsa nyengo, ndipo dzuŵa limadziŵa nthaŵi yake yoloŵera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Mwezi umasiyanitsa nyengo ndipo dzuwa limadziwa nthawi yake yolowera.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:19
9 Mawu Ofanana  

Kodi walamulira m'mawa chiyambire masiku ako, ndi kudziwitsa mbandakucha malo ake;


Kutuluka kwake lituluka kolekezera thambo, ndipo kuzungulira kwake lifikira ku malekezero ake; ndipo kulibe kanthu kobisalira kutentha kwake.


Usana ndi wanu, usikunso ndi wanu, munakonza kuunika ndi dzuwa.


Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika,


Yehova atero, amene apatsa dzuwa kuti liunikire usana, ndi malemba a mwezi ndi a nyenyezi kuti aunikire usiku, amene atonthoza nyanja, pamene mafunde ake agavira; Yehova wa makamu ndi dzina lake:


ndi kuti mungakweze maso anu kupenya kumwamba, ndipo poona dzuwa ndi mwezi ndi nyenyezi, khamu lonse la kumwamba, munganyengedwe ndi kuzigwadira, ndi kuzitumikira, zimene Yehova Mulungu wanu anagawira mitundu yonse ya anthu pansi pa thambo lonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa