Masalimo 104:18 - Buku Lopatulika18 Mapiri aatali ndiwo ayenera zinkhoma; pamatanthwe mpothawirapo mbira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Mapiri atali ndiwo ayenera zinkhoma; pamatanthwe mpothawirapo mbira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 M'mapiri aatali ndimo m'mene mumakhala mbalale, m'matanthwe ndimo m'mene mumathaŵira mbira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mapiri ataliatali ndi a mbalale; mʼmingʼalu ya miyala ndi mobisalamo mbira. Onani mutuwo |