Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 104:17 - Buku Lopatulika

17 m'mwemo mbalame zimanga zisa zao; pokhala chumba mpa mitengo ya mikungudza.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 m'mwemo mbalame zimanga zisa zao; pokhala chumba mpa mitengo ya mikungudza.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Mbalame zimamanga zisa m'menemo, dokowe amamanga chisa m'mikungudzamo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Mbalame zimamanga zisa zawo; kakowa ali ndi malo ake mʼmikungudzamo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:17
8 Mawu Ofanana  

Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, zimaimba pakati pa mitawi.


Iwe wokhala mu Lebanoni, womanga chisa chako m'mikungudza, udzachitidwa chisoni chachikulu nanga pamene mapweteko adzadza kwa iwe, monga mkazi alinkudwala!


Inde, chumba cha mlengalenga chidziwa nyengo zake; ndipo njiwa ndi namzeze ndi chingalu ziyang'anira nyengo yakufika kwao; koma anthu anga sadziwa chiweruziro cha Yehova.


Mbalame zonse za m'mlengalenga zinamanga zisa zao pa nthambi zake, ndi pansi pa nthawi zake zinaswana nyama zonse zakuthengo, ndi pa mthunzi wake inakhala mitundu yonse yaikulu ya anthu.


umene masamba ake anali okoma, ndi zipatso zake zochuluka, ndi m'menemo munali chakudya chofikira onse, umene nyama zakuthengo zinakhala pansi pake, ndi mbalame za m'mlengalenga zinapeza pokhala pao pa nthambi yake;


indwa, ndi chimeza monga mwa mtundu wake, ndi sadzu, ndi mleme.


Chinkana ukwera pamwamba penipeni ngati chiombankhanga, chinkana chisanja chako chisanjika pakati pa nyenyezi, ndidzakutsitsa kumeneko, ati Yehova.


kamene kakhaladi kakang'ono koposa mbeu zonse, koma katakula, kali kakakulu kuposa zitsamba zonse, nukhala mtengo, kotero kuti mbalame za mlengalenga zimadza, nkubindikira mu nthambi zake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa