Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 104:16 - Buku Lopatulika

16 Mitengo ya Yehova yadzala ndi madzi; mikungudza ya ku Lebanoni imene anaioka;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Mitengo ya Yehova yadzala ndi madzi; mikungudza ya ku Lebanoni imene anaioka;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Mitengo ya Chauta amaithirira ndi madzi ambiri, mikungudza ya ku Lebanoni imene adaibzala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Mitengo ya Yehova ndi yothiriridwa bwino, mikungudza ya ku Lebanoni imene Iye anadzala.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 104:16
4 Mawu Ofanana  

Liu la Yehova lithyola mitengo yamkungudza; inde Yehova athyola mikungudza ya ku Lebanoni.


Kuonetsera chifundo chanu mamawa, ndi chikhulupiriko chanu usiku uliwonse.


paphiri lothuvuka la Israele ndidzaioka, ndipo idzaphuka nthambi ndi kubala zipatso, nidzakhala mkungudza wokoma, ndi m'munsi mwake mudzakhala mbalame zilizonse za mapiko aliwonse; mu mthunzi wa nthambi zake zidzabindikira.


Ziyalika monga zigwa, monga minda m'mphepete mwa nyanja, monga khonje wooka Yehova, monga mikungudza m'mphepete mwa madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa