Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 9:48 - Buku Lopatulika

48 kumeneko mphutsi yao siikufa, ndi moto suzimidwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 kumeneko mphutsi yao siikufa, ndi moto suzimidwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Kumeneko mphutsi zoŵazunza sizifa, moto wakenso woŵatentha suzima.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 kumene “ ‘mphutsi zake sizifa ndipo moto wake suzima.’

Onani mutuwo Koperani




Marko 9:48
7 Mawu Ofanana  

Ndipo iwo adzatuluka ndi kuyang'ana mitembo ya anthu amene andilakwira Ine, pakuti mphutsi yao sidzafa, pena moto wao sudzazimidwa; ndipo iwo adzanyansa anthu onse.


Mudzidulire nokha kwa Yehova, chotsani khungu la mitima yanu, amuna inu a Yuda ndi okhala mu Yerusalemu; ukali wanga ungatuluke ngati moto, ungatenthe kuti sangathe kuuzima, chifukwa cha kuipa kwa machitidwe anu.


Pomwepo Iye adzanena kwa iwo a kudzanja lamanzere, Chokani kwa Ine otembereredwa inu, kumoto wa nthawi zonse wokolezedwera mdierekezi ndi angelo ake:


chouluzira chake chili m'dzanja lake, ndipo adzayeretsa padwale pake; ndipo adzasonkhanitsa tirigu wake m'nkhokwe, koma mankhusu adzatentha ndi moto wosazima.


Pakuti onse adzathiridwa mchere wamoto.


amene chouluzira chake chili m'dzanja lake, kuti ayeretse padwale pake, ndi kusonkhanitsa tirigu m'nkhokwe yake; koma mankhusu adzatentha m'moto wosazima.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa