Marko 9:40 - Buku Lopatulika40 Pakuti iye wosatsutsana ndi ife athandizana nafe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Pakuti iye wosatsutsana ndi ife athandizana nafe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Chifukwa wosatsutsana nafe, ndi wogwirizana nafe ameneyo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 pakuti aliyense amene satsutsana nafe ali mbali yathu. Onani mutuwo |