Marko 9:39 - Buku Lopatulika39 Koma Yesu anati, Musamamletsa iye; pakuti palibe munthu adzachita champhamvu m'dzina langa, nadzakhoza msanga kundinenera Ine zoipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Koma Yesu anati, Musamamletsa iye; pakuti palibe munthu adzachita champhamvu m'dzina langa, nadzakhoza msanga kundinenera Ine zoipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Koma Yesu adati, “Musamletse ai, chifukwa munthu sangati atachita zamphamvu m'dzina langa, nthaŵi yomweyo nkundinyoza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Yesu anati, “Musamuletse, palibe amene amachita chodabwitsa mʼdzina langa ndipo kenaka nanena zoyipa za Ine, Onani mutuwo |