Marko 9:36 - Buku Lopatulika36 Ndipo anatenga kamwana, nakaika pakati pao, nakayangata, nanena nao, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Ndipo anatenga kamwana, nakaika pakati pao, nakayangata, nanena nao, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Atatero adatenga mwana, namkhazika pakati pao nkumufungata, naŵauza kuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 Anatenga kamwana nakayimiritsa pakati pawo ndipo anawawuza kuti, Onani mutuwo |