Marko 9:30 - Buku Lopatulika30 Ndipo anachoka iwo kumeneko, napyola pakati pa Galileya; ndipo Iye sanafune kuti munthu adziwe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndipo anachoka iwo kumeneko, napyola pakati pa Galileya; ndipo Iye sanafune kuti munthu adziwe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Atachoka kumeneko, Yesu ndi ophunzira ake ankadutsa m'dziko la Galileya. Koma Iye sadafune kuti anthu adziŵe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Anachoka malo amenewo nadutsa ku Galileya. Yesu sanafune kuti wina aliyense adziwe kumene anali, Onani mutuwo |