Marko 8:37 - Buku Lopatulika37 Pakuti munthu akapereka chiyani chosintha nacho moyo wake? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201437 Pakuti munthu akapereka chiyani chosintha nacho moyo wake? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa37 Munthu angalipire chiyani choti aombolere moyo wake? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero37 Kapena nʼchiyani chomwe munthu angapereke chosinthana ndi moyo wake? Onani mutuwo |