Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 7:36 - Buku Lopatulika

36 Ndipo anawalamulira kuti asauze munthu aliyense; koma monga momwe Iye anawalamulitsa momwenso makamaka analalikira kopambana.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 Ndipo anawalamulira kuti asauze munthu aliyense; koma monga momwe Iye anawalamulitsa momwenso makamaka analalikira kopambana.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Yesu adalamula anzake a munthuyo kuti, “Musakauzetu wina aliyense zimenezi.” Koma ngakhale adaŵaletsa mwamphamvu choncho, iwo adanka nalengeza ndithu zimenezi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Yesu anawalamula kuti asawuze wina aliyense. Koma pamene anapitiriza kuwaletsa, iwo anapitiriza kuyankhula za izi.

Onani mutuwo Koperani




Marko 7:36
8 Mawu Ofanana  

Ndipo Yesu ananena naye, Ona, iwe, usauze munthu; koma muka, udzionetse wekha kwa wansembe, nupereke mtulo umene anaulamulira Mose, ukhale mboni kwa iwo.


Ndipo anailimbitsira mau kuti isamuulule Iye.


Ndipo anawalamulira kwambiri kuti asadziwe ichi munthu mmodzi, nawauza kuti ampatse iye kudya.


Ndipo makutu ake anatseguka, ndi chomangira lilime lake chinamasulidwa, ndipo analankhula chilunjikire.


Ndipo anadabwa kwakukulukulu, nanena, Wachita Iye zonse bwino; angakhale ogontha awamvetsa, ndi osalankhula awalankhulitsa.


Ndipo anamtumiza amuke kwao, nanena, Usalowe konse m'mudzi.


Ndipo pakutsika iwo paphiri, Iye anawalamula kuti asauze munthu zinthu zimene adaziona, koma pamene Mwana wa Munthu akadzauka kwa akufa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa