Marko 7:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo makutu ake anatseguka, ndi chomangira lilime lake chinamasulidwa, ndipo analankhula chilunjikire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo makutu ake anatsegula, ndi chomangira lilime lake chinamasulidwa, ndipo analankhula chilunjikire. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Pomwepo makutu a munthuyo adatsekuka, ndipo chimene chinkamanga lilime lake chidamasuka, mpaka adayamba kulankhula bwino lomwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Atachita izi, makutu a munthuyo anatsekuka komanso lilime lake linamasuka ndipo anayamba kuyankhula momveka bwino. Onani mutuwo |