Marko 6:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo Iye anakwera, nalowa kwa iwo m'ngalawa, ndipo mphepo inaleka; ndipo anadabwa kwakukulu mwa iwo okha; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo Iye anakwera, nalowa kwa iwo m'ngalawa, ndipo mphepo inaleka; ndipo anadabwa kwakukulu mwa iwo okha; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Pamenepo adaloŵa m'chombomo, mphepo nkuleka. Iwowo adathedwa nzeru kwabasi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Ndipo Iye anakwera mʼbwato pamodzi nawo, ndipo mphepo inaleka. Iwo anadabwa kwambiri, Onani mutuwo |