Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:49 - Buku Lopatulika

49 koma iwo, pamene anamuona alikuyenda panyanja, anayesa kuti ndi mzukwa, nafuula:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

49 koma iwo, pamene anamuona alikuyenda panyanja, anayesa kuti ndi mzukwa, nafuula:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

49 Koma ophunzira aja, pomuwona akuyenda pa madzi, adaaganiza kuti ndi mzukwa, nayamba kukuwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

49 koma atamuona Iye akuyenda pa nyanja, anaganiza kuti anali mzukwa. Iwo anafuwula,

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:49
6 Mawu Ofanana  

Woyala thambo yekha, naponda pa mafunde a panyanja.


Ndipo pakuwaona ali kuvutidwa ndi kupalasa, pakuti mphepo inadza nikomana nao, pa ulonda wachinai wa usiku Iye anadza kwa iwo, alikuyenda pamwamba pa nyanja; nati awapitirire;


pakuti iwo onse anamuona Iye, nanthunthumira. Koma pomwepo anawalankhula nanena nao, Limbani mtima; ndinetu, musaope.


Koma anaopsedwa ndi kuchita mantha, nayesa alikuona mzimu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa