Marko 6:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo pofika madzulo ngalawa inali pakati pa nyanja, ndi Iye yekha pamtunda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo pofika madzulo ngalawa inali pakati pa nyanja, ndi Iye yekha pamtunda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 M'mene kunkayamba kuda, nkuti chombo chija chili pakati pa nyanja, Yesu ali yekha pa mtunda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Pofika madzulo, bwato linali pakati pa nyanja, ndipo Iye anali yekha pa mtunda. Onani mutuwo |