Marko 6:45 - Buku Lopatulika45 Ndipo pomwepo Iye anakakamiza ophunzira ake alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera kutsidya lija ku Betsaida, m'mene Iye yekha alimkuuza khamulo kuti amuke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ndipo pomwepo Iye anakakamiza ophunzira ake alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera kutsidya lija ku Betsaida, m'mene Iye yekha alimkuuza khamulo kuti amuke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Madzulo omwewo Yesu adalamula ophunzira ake kuti aloŵe m'chombo, atsogole kunka ku tsidya la ku Betsaida, pamene Iye akuuza anthu kuti azipita kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 Nthawi yomweyo Yesu anawuza ophunzira ake kuti alowe mʼbwato ndi kuti atsogole kupita ku Betisaida, pamene Iye ankawuza anthu kuti azipita. Onani mutuwo |