Marko 6:43 - Buku Lopatulika43 Ndipo anatola makombo, madengu khumi ndi iwiri, ndiponso za nsomba. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201443 Ndipo anatola makombo, madengu khumi ndi iwiri, ndiponso za nsomba. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa43 Pambuyo pake ophunzira aja adatola zotsala za buledi ndi za nsomba zija nkudzaza madengu khumi ndi aŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero43 ndipo ophunzira ake anatola buledi ndi nsomba zotsalira zokwanira madengu khumi ndi awiri. Onani mutuwo |