Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:42 - Buku Lopatulika

42 Ndipo anadya iwo onse, nakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

42 Ndipo anadya iwo onse, nakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

42 Anthu onse aja adadya mpaka kukhuta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

42 Onse anadya ndipo anakhuta,

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:42
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Iye anatenga mikate isanuyo ndi nsomba ziwirizo nayang'ana kumwamba, nadalitsa, nagawa mikate; napatsa kwa ophunzira kuti apereke kwa iwo; ndi nsomba ziwiri anagawira onsewo.


Ndipo anatola makombo, madengu khumi ndi iwiri, ndiponso za nsomba.


Ndipo anadya, nakhuta onsewo; natola makombo, madengu khumi ndi awiri.


Ndipo pamene adakhuta, Iye ananena kwa ophunzira ake, Sonkhanitsani makombo kuti kasatayike kanthu.


Ndipo anakuchepetsani, nakumvetsani njala, nakudyetsani ndi mana, amene simunawadziwe, angakhale makolo anu sanawadziwe; kuti akudziwitseni kuti munthu sakhala wamoyo ndi mkate wokha, koma munthu akhala wamoyo ndi zonse zakutuluka m'kamwa mwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa