Marko 6:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo anakhala pansi mabungwemabungwe a makumi khumi, ndi a makumi asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo anakhala pansi mabungwemabungwe a makumi khumi, ndi a makumi asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Anthu aja adakhaladi pansi, m'magulu mwina anthu makumi khumi, mwina anthu makumi asanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Ndipo anakhala pansi mʼmagulu a anthu 100 ndi gulu la anthu makumi asanu. Onani mutuwo |