Marko 6:39 - Buku Lopatulika39 Ndipo anawalamulira kuti akhalitse pansi onse magulumagulu pamsipu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201439 Ndipo anawalamulira kuti akhalitse pansi onse magulumagulu pamsipu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa39 Tsono Yesu adalamula kuti anthu onse aja akhale pansi m'magulumagulu pa msipu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero39 Pamenepo Yesu anawalamulira kuti awakhazike anthu pansi mʼmagulu pa msipu obiriwira. Onani mutuwo |