Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:36 - Buku Lopatulika

36 muwauze kuti amuke, alowe kuminda ndi kumidzi yozungulira, akadzigulire okha kanthu kakudya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

36 muwauze kuti amuke, alowe kumilaga ndi kumidzi yozungulira, akadzigulire okha kanthu kakudya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

36 Auzeni anthuŵa azipita, anke ku midzi ili pafupiyi kuti azikagula chakudya.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

36 Awuzeni anthuwa azipita ku midzi ndi madera ozungulira, kuti akadzigulire kanthu kakuti adye.”

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:36
6 Mawu Ofanana  

Koma Iye sanamyankhe mau amodzi. Ndipo ophunzira ake anadza, nampempha, nati, Mumuuze amuke; pakuti afuula pambuyo pathu.


Ndipo Petro anamtenga Iye, nayamba kumdzudzula, kuti, Dzichitireni chifundo, Ambuye; sichidzatero kwa Inu ai.


Ndipo pamene abale ake anamva, anadza kudzamgwira Iye; pakuti anati adayaluka.


Ndipo ophunzira ake ananena kwa Iye, Muona kuti khamu lilikukanikiza Inu, ndipo munena kodi, Wandikhudza ndani?


Ndipo pamene dzuwa lidapendeka ndithu, anadza kwa Iye ophunzira ake, nanena, Malo ano nga chipululu, ndi dzuwa lapendeka ndithu;


Koma Iye anayankha nati kwa iwo, Apatseni kudya ndinu. Ndipo iwo ananena naye, Kodi tikapita ife ndi kugula mikate ya pa marupiya atheka mazana awiri, ndi kuwapatsa kudya?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa