Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:32 - Buku Lopatulika

32 Ndipo anachokera m'ngalawa kunka kumalo achipululu padera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Ndipo anachokera m'ngalawa kunka kumalo achipululu padera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Tsono adaloŵa m'chombo napita kwaokha kumalo kosapitapita anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ndipo anachoka okha pa bwato napita kumalo a okhaokha.

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:32
10 Mawu Ofanana  

Ndipo anati kwa ophunzira ake, kuti kangalawa kamlinde Iye, chifukwa cha khamulo, kuti angamkanikize Iye,


Ndipo posiya khamulo anamtenga apite nao, monga momwe anali, mungalawa. Ndipo panali ngalawa zina pamodzi ndi Iye.


Ndipo anthu anawaona alikumuka, ndipo ambiri anawazindikira, nathamangira limodzi kumeneko pamtunda, ochokera m'midzi monse, nawapitirira.


Ndipo pomwepo Iye anakakamiza ophunzira ake alowe m'ngalawa, ndi kumtsogolera kutsidya lija ku Betsaida, m'mene Iye yekha alimkuuza khamulo kuti amuke.


Ndipo Iye anakwera, nalowa kwa iwo m'ngalawa, ndipo mphepo inaleka; ndipo anadabwa kwakukulu mwa iwo okha;


Zitapita izi anachoka Yesu kunka kutsidya lija la nyanja ya Galileya, ndiyo ya Tiberiasi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa