Marko 6:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo m'mene ophunzira ake anamva, anadza nanyamula mtembo wake nauika m'manda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo m'mene ophunzira ake anamva, anadza nanyamula mtembo wake nauika m'manda. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Ophunzira a Yohane atamva zimenezi, adabwera nadzatenga mtembo wake nkukauika m'manda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Atamva izi, ophunzira a Yohane anabwera nadzatenga mtembo ndi kukawuyika mʼmanda. Onani mutuwo |