Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Marko 6:27 - Buku Lopatulika

27 Ndipo pomwepo mfumu inatuma mnyamata, namlamulira akatenge mutu wake; ndipo iye anamuka namdula mutu m'nyumba yandende;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndipo pomwepo mfumu inatuma mnyamata, namlamulira akatenge mutu wake; ndipo iye anamuka namdula mutu m'nyumba yandende;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Choncho nthaŵi yomweyo adatuma mmodzi mwa asilikali ake, namulamula kuti abwere nawo mutu wa Yohanewo. Msilikaliyo adapita ku ndende, nakamdula mutu Yohaneyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Nthawi yomweyo iye anatumiza yemwe anali ndi ulamuliro wonyonga anthu kuti abweretse mutu wa Yohane. Munthuyo anapita, nakadula mutu wa Yohane mʼndende,

Onani mutuwo Koperani




Marko 6:27
3 Mawu Ofanana  

Ndipo mfumu inamva chisoni chachikulu; koma chifukwa cha malumbiro ake, ndi cha iwo akukhala pachakudya, sanafune kumkaniza.


natengera mutu wake mumbale, naupereka kwa buthulo; ndipo buthu linaupereka kwa amake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa