Marko 6:26 - Buku Lopatulika26 Ndipo mfumu inamva chisoni chachikulu; koma chifukwa cha malumbiro ake, ndi cha iwo akukhala pachakudya, sanafune kumkaniza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndipo mfumu inamva chisoni chachikulu; koma chifukwa cha malumbiro ake, ndi cha iwo akukhala pachakudya, sanafune kumkaniza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Pamenepo mfumu Herode adamva chisoni kwambiri. Koma chifukwa cha malumbiro ake ndiponso chifukwa cha anthu oitanidwa ku phwando aja, sadafune kuphwanya lonjezo lake kwa mtsikanayo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mfumu inamva chisoni chachikulu, koma chifukwa cha lumbiro lake ndi alendo ake a pa mphwandolo, sanafune kumukaniza. Onani mutuwo |